Aheberi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyu wakhala wotero, osati malinga ndi zofunika za chilamulo, chimene chimadalira zinthu za padziko lapansi,+ koma malinga ndi mphamvu imene imapatsa moyo wosakhoza kuwonongeka.+
16 Iyeyu wakhala wotero, osati malinga ndi zofunika za chilamulo, chimene chimadalira zinthu za padziko lapansi,+ koma malinga ndi mphamvu imene imapatsa moyo wosakhoza kuwonongeka.+