Aheberi 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zikanakhala choncho, kodi nsembezo sakanasiya kuzipereka? Akanasiya chifukwa chakuti anthu ochita utumiki wopatulika, amene akanayeretsedwa kwathunthu kamodzi n’kamodziwo, sakanakhalanso ndi chikumbumtima chakuti ndi ochimwa.+
2 Zikanakhala choncho, kodi nsembezo sakanasiya kuzipereka? Akanasiya chifukwa chakuti anthu ochita utumiki wopatulika, amene akanayeretsedwa kwathunthu kamodzi n’kamodziwo, sakanakhalanso ndi chikumbumtima chakuti ndi ochimwa.+