Aheberi 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+
33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+