1 Yohane 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati tinena kuti: “Ndife ogwirizana naye,” koma tikupitiriza kuyenda mu mdima,+ ndiye kuti tikunama ndipo sitikuchita choonadi.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,8/1/1991, tsa. 171/15/1987, tsa. 27
6 Ngati tinena kuti: “Ndife ogwirizana naye,” koma tikupitiriza kuyenda mu mdima,+ ndiye kuti tikunama ndipo sitikuchita choonadi.+