1 Yohane 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2020, tsa. 24 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, tsa. 32
17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+