Chivumbulutso 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 131
5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+