Chivumbulutso 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266
6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+