CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MLALIKI 7-12
“Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”
Muzikumbukira Mlengi Wanu Wamkulu pogwiritsa ntchito mphamvu zanu pomutumikira mudakali achinyamata
Achinyamata ambiri ndi athanzi komanso amphamvu moti akhoza kugwira ntchito zovuta
Achinyamata ayenera kugwiritsa ntchito nthawi komanso mphamvu zawo potumikira Mulungu asanayambe kukumana ndi mavuto obwera chifukwa cha ukalamba