Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Genesis 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+ Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+ Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+