-
Genesis 14:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pambuyo pake, munthu wina amene anathawa anafika kwa Abulamu Mheberi.+ Pa nthawiyo n’kuti Abulamu akukhala m’hema wake pakati pa mitengo ikuluikulu. Mitengoyo mwiniwake anali Mamure, yemwe anali Muamori.+ Ameneyu anali m’bale wake wa Esikolo, ndipo analinso m’bale wake wa Aneri.+ Iwowa anapanga ubale ndi Abulamu.
-