-
Aheberi 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mwa chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Mwa chikhulupiriro chimenecho, anatsutsa dziko,+ ndipo anakhala wolandira cholowa cha chilungamo,+ chimene chimabwera ndi chikhulupiriro.
-