Ekisodo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo ana aamuna a Kora anali Asiri, Elikana ndi Abiasafu.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Kora.+ Numeri 26:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Nawa mabanja a Alevi: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi,+ ndi banja la Akora.+ Kohati+ anabereka Amuramu.+ Salimo 42:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Kwa wotsogolera nyimbo. Masikili* ya ana a Kora.+ Salimo 45:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Kwa wotsogolera nyimbo pa Maluwa.* Salimo la ana a Kora. Masikili.* Nyimbo yonena za akazi okondedwa.
58 Nawa mabanja a Alevi: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi,+ ndi banja la Akora.+ Kohati+ anabereka Amuramu.+
Kwa wotsogolera nyimbo pa Maluwa.* Salimo la ana a Kora. Masikili.* Nyimbo yonena za akazi okondedwa.