8 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Inetu ndakupatsa udindo woyang’anira zopereka zonse zoperekedwa kwa ine.+ Pa zinthu zonse zopatulika zimene ana a Isiraeli azipereka, ndakupatsako gawo iweyo ndi ana ako, likhale gawo lanu mpaka kalekale.+