Genesis 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inuyotu munanena kuti, ‘Mosakayikira m’pang’ono pomwe ndidzakusamalira, ndipo ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa kunyanja, umene suwerengeka kuchuluka kwake.’”+ Ekisodo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho nditsikira kwa iwo kuti ndiwalanditse m’manja mwa Aiguputo,+ ndi kuwatulutsa m’dzikolo, n’kuwalowetsa m’dziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi.+ Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
12 Inuyotu munanena kuti, ‘Mosakayikira m’pang’ono pomwe ndidzakusamalira, ndipo ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa kunyanja, umene suwerengeka kuchuluka kwake.’”+
8 Choncho nditsikira kwa iwo kuti ndiwalanditse m’manja mwa Aiguputo,+ ndi kuwatulutsa m’dzikolo, n’kuwalowetsa m’dziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi.+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+