2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Luka 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+