1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+ Salimo 74:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+ Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+
10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+
2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+
71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+