Deuteronomo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Abambo asaphedwe chifukwa cha machimo a ana, ndipo ana asaphedwe chifukwa cha machimo a abambo.+ Aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.+ 1 Samueli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo m’nyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ M’nyumba yako simudzapezeka munthu wokalamba.
16 “Abambo asaphedwe chifukwa cha machimo a ana, ndipo ana asaphedwe chifukwa cha machimo a abambo.+ Aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.+
32 Ndipo m’nyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ M’nyumba yako simudzapezeka munthu wokalamba.