Deuteronomo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ukapereka lonjezo kwa Yehova+ Mulungu wako usachedwe kulikwaniritsa kuopera kuti ungachimwe,+ chifukwa Yehova Mulungu wako adzafuna ndithu kuti ukwaniritse chimene walonjezacho.+ Oweruza 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno iye anapempha amuna a ku Sukoti+ kuti: “Chonde, patsaniko anthu amene akunditsatirawa+ mitanda yobulungira ya mkate chifukwa ndi otopa, pakuti ndikuthamangitsa Zeba+ ndi Zalimuna,+ mafumu a Midiyani.” 2 Samueli 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anabweretsanso uchi,+ mafuta a mkaka,+ wa ng’ombe ndiponso nkhosa. Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo anali kunena kuti: “Anthu amenewa ali ndi njala, atopa ndipo ali ndi ludzu m’chipululu.”+ Salimo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+
21 “Ukapereka lonjezo kwa Yehova+ Mulungu wako usachedwe kulikwaniritsa kuopera kuti ungachimwe,+ chifukwa Yehova Mulungu wako adzafuna ndithu kuti ukwaniritse chimene walonjezacho.+
5 Ndiyeno iye anapempha amuna a ku Sukoti+ kuti: “Chonde, patsaniko anthu amene akunditsatirawa+ mitanda yobulungira ya mkate chifukwa ndi otopa, pakuti ndikuthamangitsa Zeba+ ndi Zalimuna,+ mafumu a Midiyani.”
29 Iwo anabweretsanso uchi,+ mafuta a mkaka,+ wa ng’ombe ndiponso nkhosa. Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo anali kunena kuti: “Anthu amenewa ali ndi njala, atopa ndipo ali ndi ludzu m’chipululu.”+
4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+