Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+ Levitiko 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi. Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Choncho mudzipatule monga anthu oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+
44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.