1 Samueli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti. 2 Samueli 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’kalatamo analembamo kuti:+ “Muike Uriya kutsogolo kumene nkhondo yakula,+ ndipo inu mubwerere m’mbuyo kuti amukanthe ndipo afe ndithu.”+ 2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni. Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+
25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti.
15 M’kalatamo analembamo kuti:+ “Muike Uriya kutsogolo kumene nkhondo yakula,+ ndipo inu mubwerere m’mbuyo kuti amukanthe ndipo afe ndithu.”+
9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.