-
1 Mafumu 2:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ukatero, Yehova adzabwezeradi pamutu pake magazi ake,+ chifukwa anakantha amuna awiri olungama ndi abwino kuposa iyeyo,+ ndipo anawapha ndi lupanga. Anachita zimenezi Davide bambo anga osadziwa.+ Amuna ake anali Abineri+ mwana wa Nera mkulu wa asilikali a Isiraeli,+ ndi Amasa+ mwana wa Yeteri mkulu wa asilikali a Yuda.+
-