1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi. 2 Mbiri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+ Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ Miyambo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+
23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+
7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+