Oweruza 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8. Salimo 69:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa. Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake. Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.
26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa.
5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake.
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+