Yesaya 54:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mkwiyo waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+ koma ndidzakuchitira chifundo+ ndiponso ndidzakusonyeza kukoma mtima kosatha mpaka kalekale,” watero Yehova, Wokuwombola.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+
8 Ndi mkwiyo waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+ koma ndidzakuchitira chifundo+ ndiponso ndidzakusonyeza kukoma mtima kosatha mpaka kalekale,” watero Yehova, Wokuwombola.+
7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+