5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+
16 Ndasankha+ ndi kuyeretsa nyumba ino kuti dzina langa+ likhale pamenepa mpaka kalekale,+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+