Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+ Salimo 68:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 N’chifukwa chiyani inu mapiri a nsonga zitalizitali mumayang’ana mwanjiruPhiri limene Mulungu wafuna kukhalamo?+Yehova adzakhala m’phiri limenelo mpaka muyaya.+ Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+ Yoweli 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Magazi awo amene anali ndi mlandu adzakhala opanda mlandu,+ ndipo Yehova azidzakhala mu Ziyoni.”+ Zekariya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.
16 N’chifukwa chiyani inu mapiri a nsonga zitalizitali mumayang’ana mwanjiruPhiri limene Mulungu wafuna kukhalamo?+Yehova adzakhala m’phiri limenelo mpaka muyaya.+
23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+
10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.