-
Salimo 95:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+
Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+
-