Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi M’busa wanga.+Sindidzasowa kanthu.+ Salimo 48:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Mulungu uyu ndi Mulungu wathu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Iye adzatitsogolera kufikira imfa yathu.+ Salimo 79:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+ Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+ Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+ Ezekieli 34:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu ochokera kufumbi. Ine ndine Mulungu wanu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
14 Pakuti Mulungu uyu ndi Mulungu wathu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Iye adzatitsogolera kufikira imfa yathu.+
13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+
31 “‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu ochokera kufumbi. Ine ndine Mulungu wanu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”