Yobu 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye akachititsa bata, ndani angamudzudzule?Ndipo akabisa nkhope yake,+ ndani angamuone?Kaya abisire nkhope yake mtundu+ kapena munthu, n’chimodzimodzi. Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+ Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+ Salimo 69:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+ Salimo 88:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani mukunditaya?+N’chifukwa chiyani mukundibisira nkhope yanu?+ Maliro 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+
29 Iye akachititsa bata, ndani angamudzudzule?Ndipo akabisa nkhope yake,+ ndani angamuone?Kaya abisire nkhope yake mtundu+ kapena munthu, n’chimodzimodzi.
13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+
9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+
17 Ndipo ine mtumiki wanu musandibisire nkhope yanu.+Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndasautsika kwambiri.+
20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+