Deuteronomo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+ Aheberi 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.
10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+
38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.