Salimo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti akufa satchula za inu.+Kodi ndani angatamande inu ali m’Manda?*+ Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+ Salimo 118:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindidzafa, koma ndidzakhalabe ndi moyo,+Kuti ndilengeze ntchito za Ya.+ Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+ Yesaya 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+
9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+
5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+
18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+