Genesis 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai,+ Yavani,+ Tubala,+ Meseke+ ndi Tirasi.+ Ezekieli 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.
13 Iwe unali kuchita malonda ndi Yavani,+ Tubala+ ndi Meseke.+ Unali kuwapatsa katundu wako wogulitsa pomusinthanitsa ndi anthu+ komanso zinthu zamkuwa.