2 Samueli 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli. 2 Mbiri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu. Miyambo 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+ Agalatiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Kefa+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamutsutsa pamasom’pamaso, chifukwa anali wolakwa.+ Agalatiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abale, ngati munthu wapatuka n’kuyamba kulowera njira yolakwika+ mosazindikira, inu oyenerera mwauzimu,+ yesani kumuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Pamene mukutero, aliyense wa inu asamale,+ kuopera kuti iyenso angayesedwe.+
7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli.
7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu.
10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+
6 Abale, ngati munthu wapatuka n’kuyamba kulowera njira yolakwika+ mosazindikira, inu oyenerera mwauzimu,+ yesani kumuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Pamene mukutero, aliyense wa inu asamale,+ kuopera kuti iyenso angayesedwe.+