1 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+ Salimo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova wanena kuti: “Chifukwa cha kuponderezedwa kwa osautsika, chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka pa nthawiyo,+Ndidzawateteza kwa aliyense wowanyodola.”+ Miyambo 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Wowawombola ndi wamphamvu, ndipo adzawateteza pa mlandu wawo ndi iwe.+ Yeremiya 50:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Wowawombola ndi wamphamvu,+ dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo+ kuti apumitse dziko lawo+ ndiponso kusokoneza mtendere wa anthu okhala m’Babulo.”+ Mika 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+
12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+
5 Tsopano Yehova wanena kuti: “Chifukwa cha kuponderezedwa kwa osautsika, chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka pa nthawiyo,+Ndidzawateteza kwa aliyense wowanyodola.”+
34 Wowawombola ndi wamphamvu,+ dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo+ kuti apumitse dziko lawo+ ndiponso kusokoneza mtendere wa anthu okhala m’Babulo.”+
9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+