Miyambo 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pali munthu amene amadzionetsera kuti ndi wolemera koma alibe kalikonse.+ Ndiponso pali munthu amene amaoneka ngati wosauka koma ali ndi zinthu zambiri zamtengo wapatali. Luka 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti aliyense wodzikweza adzatsitsidwa, ndipo wodzichepetsa adzakwezedwa.”+
7 Pali munthu amene amadzionetsera kuti ndi wolemera koma alibe kalikonse.+ Ndiponso pali munthu amene amaoneka ngati wosauka koma ali ndi zinthu zambiri zamtengo wapatali.