Mlaliki 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinafufuza ndi mtima wanga wonse kuti ndidziwe uchitsiru posangalatsa thupi langa ndi vinyo,+ pamene ndinali kutsogolera mtima wanga ndi nzeru.+ Ndinachita zimenezi kuti ndione ubwino umene ana a anthu amapeza pa zimene amachita padziko lapansi pano masiku onse a moyo wawo.+ Mlaliki 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+ Mlaliki 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ntchentche zakufa n’zimene zimachititsa mafuta onunkhira oyengedwa bwino+ kuwola ndi kuyamba kununkha. Momwemonso uchitsiru pang’ono umawononga mbiri ya munthu amene akulemekezedwa chifukwa cha nzeru ndi ulemerero wake.+
3 Ndinafufuza ndi mtima wanga wonse kuti ndidziwe uchitsiru posangalatsa thupi langa ndi vinyo,+ pamene ndinali kutsogolera mtima wanga ndi nzeru.+ Ndinachita zimenezi kuti ndione ubwino umene ana a anthu amapeza pa zimene amachita padziko lapansi pano masiku onse a moyo wawo.+
25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+
10 Ntchentche zakufa n’zimene zimachititsa mafuta onunkhira oyengedwa bwino+ kuwola ndi kuyamba kununkha. Momwemonso uchitsiru pang’ono umawononga mbiri ya munthu amene akulemekezedwa chifukwa cha nzeru ndi ulemerero wake.+