Miyambo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma zili ngati mudzi wake wolimba.+ Chiwonongeko cha onyozeka ndicho umphawi wawo.+ Maliko 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Yohane 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Palibe ndi mmodzi yemwe mwa olamulira kapena Afarisi amene wakhulupirira mwa iye, alipo ngati?+ 1 Akorinto 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu. 1 Akorinto 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.
15 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma zili ngati mudzi wake wolimba.+ Chiwonongeko cha onyozeka ndicho umphawi wawo.+
3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+
27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu.
8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.