Salimo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Salimo 107:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+ Salimo 145:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo,+Ndipo adzasimba za zochita zanu zamphamvu.+
5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+
8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+