Salimo 125:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+ Yesaya 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+ Zekariya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsiku limenelo, Yehova adzatchinjiriza anthu okhala mu Yerusalemu.+ Munthu amene wapunthwa pa tsiku limenelo, adzakhala wamphamvu ngati Davide.+ Nyumba ya Davide idzawatsogolera ngati Mulungu,+ ndiponso ngati mngelo wa Yehova.+
125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+
13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+
8 Pa tsiku limenelo, Yehova adzatchinjiriza anthu okhala mu Yerusalemu.+ Munthu amene wapunthwa pa tsiku limenelo, adzakhala wamphamvu ngati Davide.+ Nyumba ya Davide idzawatsogolera ngati Mulungu,+ ndiponso ngati mngelo wa Yehova.+