Salimo 45:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+ Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+ Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+
6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+
6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+
5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+