Miyambo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usakhale pakati pa anthu omwa vinyo kwambiri,+ ndiponso pakati pa anthu odya nyama mosusuka.+ Miyambo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa angamwe n’kuiwala malamulo ndi kupondereza ufulu wa ana ovutika.+ Yesaya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka m’mawa kuti akafunefune chakumwa choledzeretsa.+ Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.+
11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka m’mawa kuti akafunefune chakumwa choledzeretsa.+ Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.+