-
Danieli 4:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 “‘Chifukwa chakuti inu mfumu munaona mlonda woyera+ akutsika kuchokera kumwamba, akunena kuti: “Gwetsani mtengowo ndipo muuwononge, koma musiye chitsa chake munthaka, mutachikulunga ndi mkombero wachitsulo ndi wamkuwa, chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba, chikhale limodzi ndi nyama zakutchire kufikira patadutsa nthawi zokwanira 7,”+
-