2 Mafumu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeliwo sanamvere+ mawu a Yehova Mulungu wawo, koma anaphwanya pangano lake,+ ngakhalenso zonse zimene Mose+ mtumiki wa Yehova anawalamula.+ Iwo sanamvere kapena kuzichita. Ezekieli 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+ Nahumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+
12 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeliwo sanamvere+ mawu a Yehova Mulungu wawo, koma anaphwanya pangano lake,+ ngakhalenso zonse zimene Mose+ mtumiki wa Yehova anawalamula.+ Iwo sanamvere kapena kuzichita.
38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+