Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi M’busa wanga.+Sindidzasowa kanthu.+ Salimo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+ Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+ Yohane 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nkhosa+ zanga zimamva mawu anga. Ine ndimazidziwa, ndipo izo zimanditsatira.+
9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+
11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+