-
2 Akorinto 7:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo taonani zimene chisoni chogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu+ chimenechi chakuchitirani. Chakuchititsani kukhala akhama kwambiri, chakuchititsani kudziyeretsa, kuipidwa, mantha, kufunitsitsa kulapa, kudzipereka, ndiponso kukonza cholakwacho.+ Mwanjira ina iliyonse, munasonyeza kuti ndinu oyera pa nkhani imeneyi.
-