9 iwo atazindikira kukoma mtima kwakukulu+ kumene ndinapatsidwa,+ Yakobo,+ Kefa ndi Yohane, amene anali ngati mizati,+ anagwira chanza ineyo ndi Baranaba.+ Anatero posonyeza kuti agwirizana nazo+ zoti ife tipite kwa anthu a mitundu ina, ndipo iwo apite kwa odulidwa.