Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ Machitidwe 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa lonjezo lonselo kwa ife ana awo mwa kuukitsa Yesu.+ Zimenezi n’zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala Atate wako.’+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa lonjezo lonselo kwa ife ana awo mwa kuukitsa Yesu.+ Zimenezi n’zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala Atate wako.’+