Salimo 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Mulungu adzawombola moyo wanga ku Manda,+Pakuti adzandilandira. [Seʹlah.] Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+ Machitidwe 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ Chivumbulutso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+
11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+
31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+