Afilipi 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ife ndife amdulidwe weniweni,+ amene tikuchita utumiki wopatulika mwa mzimu wa Mulungu.+ Timadzitamandira mwa Khristu Yesu,+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,+ Aheberi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?
3 Pakuti ife ndife amdulidwe weniweni,+ amene tikuchita utumiki wopatulika mwa mzimu wa Mulungu.+ Timadzitamandira mwa Khristu Yesu,+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,+
14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?