-
Aheberi 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tichite zimenezi pamene tikuyang’anitsitsa Mtumiki Wamkulu+ ndi Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu,+ Yesu. Chifukwa cha chimwemwe chimene anamuikira patsogolo pake,+ anapirira mtengo wozunzikirapo.* Iye sanasamale kuti zochititsa manyazi zimuchitikira, ndipo tsopano wakhala pansi kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu.+
-